Galimoto Ya Asaulos Chilima Yabedwa

preview_player
Показать описание
ZANGAZANGA CHIKHOSI ABA GALIMOTO ZA BOMA
Pali malipoti omwe akusonyeza kuti mlembi wakale wa president ndi nduna, a Zangazanga Chikhosi omwe anachotsedwa pa udindowu mmasiku apitawa ndi mtsogoleroi wa dziko lino, atenga galimoto zitatu zmwe sizawo koma zoti azigwiritsa ntchito amene walowa mmalo mwawo. Mwa galimoto zitatuzi, imodzi ndi yoti inagulidwa ndi cholinga choti adzigwiritsa ntchito wa chiwiri kwa mtosgoleri wa dziko lino Dr Saulos Klaus Chilima pomwe ziwiri zinazo ndi za mtundu wa Mercedes Benz ndi Toyota VX zomwe ndi zimene amagwiritsa ntchito ali pa udindo. Galimoto yomwe imayenera ikhale ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko linoyu ndi ya mtundu wa Toyota V8R Land Cruiser yomwe inagulidwa pa mtengo wa ndalama zokwana 141 million kwacha.
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

koma dzikoli ndi lanthu olemeradi et? mpaka munthu kuba chinthu cha office ya boma mpaka kurephera kumulanda???? mukutiseweretsatu makosana😂😂😂😂😂

MorganBanda-ocjx
Автор

Komatu anthu musamaone utsilu kwa omwe amavota mwauze azithenge bwino

wysonmpatama
Автор

Iwe taziyankhula bwino, usamakhale ngati mzukwa!!!

JoycieMbaya
Автор

Mizinda yanthu Umve ndi wambiri Hanifa take note of that

joeljere
Автор

Zakhala bwanji kwa anyamata oganiza bho!?

fredrickkachepa
Автор

Okuba wabedwa so don’t cry and you should feel how it is when you steal government money and corruption.

sidickbadat
visit shbcf.ru