A SHADO(Part 1)- Episode 135 ft Chisi

preview_player
Показать описание

Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

mwafika panopa kupitas Kwa mfumu NDI mistake yayikulu😂😂😂😂😂

Chifukwa chomwe chingachitke mukupita Kwa amfumuwo akuuzan Zama bigg, 2 😂😂😂😂😂😂 aaaa you guys I real enjoyed your comedy's and keep doing fantastic comedy we love it

eishmeilakidu
Автор

Watching from south africa 🇿🇦 ur best mandota

alfredbatumeyo
Автор

Kom uyu🤣🤣🤣ati mbale wanga angakhale wonyasa chocho🤣🤣🤣🙌🏻

PatriciaKhola-ykib
Автор

Koma a Chisi phuma 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂, Keep it up Mr and your brother ❤❤❤

robertrichman
Автор

Eeh eeh chisi combination iyi imandiwaza wasala m'bulundi uja

Inno-x
Автор

😂😂😂😂😂😗😚🧘‍♀️ chi mandato ndi ovuta kubwezi zinthu

lazarusedward
Автор

Achisi adzibwerabwera anasowatu Achisi dekhani Ndalama ya MA VOTE 🗳 ☑️ 🗳 ☑️ ACHISI YANU IYI CHEMANDOTA YANGA IYI HAHAHA 😆 😂 😄 🤣 💖 😀 😆

mollymasangano
Автор

koma mtumbukayu ndiye osusuka ndi ndalama bwanji 😂😂😂😂😂

ayamijackson
Автор

Anafika ngat nsilikali😂😂😂😂😂😂😂😂 aaaa wangongole

ToxAlimonjaimeJaime
Автор

Tiye nazo timakondwa nanu best comedian 2023💪💪💪

hamzahsm
Автор

😂😂😂😂😂koma chisi usandisekese 😂😂😂😂kupusa kumayandikana ndikufasa😂😂😂big up guys watching from UAE 🇦🇪 Dubai

elliottphalula
Автор

Chisi please aziyakhura chitumbukaa akuvutika kwambiri 😂😂😂😂

EdwardMahatma-rmmi
Автор

Am watching from lusaka Zambia nice video che mandota

danielchimangen
Автор

Ukanakhala AMP chemandota ukanwina ndiacchisi😅😅😅😅😅

LukeMbewa-dddb
Автор

Koma achizizotu nde akuyangura saupongweeee

frankkachigumba
Автор

Up mandota 🤍🤍 watching from Cape Town South Africa umativetsa kukoma nthawi zonse 😂😂

rashidstamburi
Автор

Kkkk akangani munakula chonchi 😂😂😅😂😅😂😅😂😅😂

richwilly
Автор

Koma zosekesa ndithu aononga nkhani azanu achemandota achisi paka kuyankhula kuti tabela maepi

slyviakalivea
Автор

Zapangilandi zampira muchedwa nazo Achisi 😂😂😂

ussimasi
Автор

Kkkkk nkhani yake itio mpaka kukumba manda

JoanMagola-poli