PEMPHERA - THOKO SUYA

preview_player
Показать описание
Songs of Hope #mundiwa
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

Spiritual song ❤❤ so edifying and we are blessed

josephmaunde
Автор

Really! Mulungu amaona komanso amayankha. Mulungu akudalitseni Mama Suya

fwasanishaba
Автор

Nyengo ziwawe, zisawawe....iwe pemphera....Yesu samagonai nthawi zonse amakhala ambuye ngoopysa chilichonse amaona...nyimbo yabwino kwambiri

kalibwilasekanawo
Автор

This song muli bvumbulutso osati za pang'ono! Mwamenya!🎉

nancymunthali
Автор

Nyimbo iyi mwakwapula mama, size kukana, Ambuye apitilize kukupasani mavumbulutso kudzera mmaimbidwe

henryphiri
Автор

Every song from you mom is my favorite ❤🎉🎉

blairmajaliwa