Phyzix - WIFE MATERIAL ft. Pon G (Official Video) 2021

preview_player
Показать описание
Phyzix, It's Only Entertainment (IOE) Artist/CEO delivers his brand new song 'WIFE MATERIAL' ft. Pon G. In association with WWE Snacks, Kelfoods, Ryalls Hotel and The Bistro.

© 2021 It's Only Entertainment (IOE)

FOLLOW PHYZIX ON SOCIAL MEDIA
(All social media profiles are verified).

Don’t forget to SUBSCRIBE to be part of our community.

A film by It's Only Entertainment (IOE)
Director: Skript
Editor: Skript
Cinematography: SeanyFilms
Photographer: Raz Mirambo
Stylist: Chip Nigga
Colorist: Skript & Seany
ARM: Eric Chan
Production Manager: King George Damson
Logistics Manager: Macmilly
Transport Manager: Evident
Location Manager: Phyzix
Audio Producer: Pon G
Music: Phyzix ft. Pon G
Creative Directors: Skript & Seany
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

*Wife Material Lyrics by Phyzix & Pon G*

*(INTRO: Phyzix)*
Kukakhala kunjaku kwacha bho... yeah/ yeah
Kukakhala kunjaku kwacha bho/ zachita kudzadzamo bobobo/ Wifey material/ terial/ terial/ Wifey ma ti ti ti ti

*(VERSE 1: Phyzix)*
Ndinapeza chibhebhi anthu adziwe/ sindimachibisa sichapadziwe/ yemwe zikumuwawa adhiwe/ koma ichichi ndi changa chi Lindiwe/ sichingazakupatse mphindi iwe chimakhala chili ndi ine uzimva iwe/ vuto lake iweyo kuzimva iwe umangogwira akazi openga ma byzwe/ Za ife ndi zokoma zothila curry/ sitimvetsana kuwawa tsabola wa kale/ Uyuyu ndi wanga si temporary/ ndikanena kuti ndimugaya si mphale/ kutentha ngati Nali samalani abale/ akusungila sugar wonyambititsa mbale/ Mkazi uyu ngoiwalitsa abale/ amakomedwetsa ngati anthu a Ndale/ Very Good Very Good

*(HOOK: Pon G & Phyzix)*
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a M'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti

*(VERSE 2: Phyzix)*
Ichi ndi chi ndiwo koma si mpiru/ sindinachite kuchiba koma ndi chi dhilu/ ichi ndi chibhebhi chodzadza feel/ dzina lake ndinaliyika kale pa will/ chimandikumbutsa Maggie Mwaupighu/ mahope anga a ku Primary ku Mphungu/ tili mafana oyankhula chizungu/ she had a chocolate skin ndimamufila khungu
Chibhebhi changachi chandipatsa khungu/ ndikayenda m'townimu sindiona buthu/ Ndadwala Chikondi 10 pa 10/ chachita kundifika pe mpeni/ Ndavomera Mami ndi malizeni/ sindipempha kuti Ambuye ndichilitseni
Izi si za gulu si za m'memo/ Ineyo ndili momo m'menemo/ Very Good Very Good

*(HOOK: Pon G & Phyzix)*
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a M'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti

*(BRIDGE: Pon G & Phyzix)*
Gal you di wife material/ I just wanna make you my wife ooh
Gal you di one in a million/ this feeling for you I can't deny ooh

Iwe ndiwe Mkazi wooneka bho/ wooneka bho/ wooneka bho
Iwe ndiwe chi Mkazi chooneka/ chooneka bho/ chooneka bho
Iwe ndi Mkazi wofitha bho/ wofitha bho/ wofitha bho
Iwe ndi chi Mkazi chofitha bho/ chofitha bho/ chofitha bho

*(HOOK: Pon G & Phyzix)*
Mami ndinu chi Mkazi chooneka bho
Mumachita kukhala ngati a M'video
Mami muli pure ngati ka viligo/ mukazafuna banja ife tilipo
Ndinu wifey material terial terial
Wifey ma ti ti ti ti
Wifey material terial terial
Wifey ti ti ti ti

Phyzix
Автор

My daughter is Lindiwe so every time she's sad I say to her ICHICHI NDICHANGA CHI LINDIWE!! Her smile is always priceless. ❤is

Magada
Автор

You are and you will always be my best Rapper in Malawi, , keep fire burning

preciouschikazingwa
Автор

Nyimbo ina iliyonse ya phyzix imakhala fire 🔥

alinafemanonga
Автор

The moment i heard about you guys this January 2024 aaa sidafune tsiku lipite nsalowe your u tube ❤

chisonimponda
Автор

Lovely Video, Lovely song too. From Zambia keep it up Neighbor

queenlicah
Автор

Phyzo mumatha & you're on the amongst of Legends in Malawi. Big biggy🔥💪✌️👌

EvelynMwanza-lywh
Автор

Powerful songs guys. Physics and Pon G you are great musicians in Malawi for sure. I can challenge you guys, if you can produce 100 tracks just Physics ft Pon G all of them should be top notch songs for sure!!

PatrickManjomo-dxky
Автор

Mmm in this song nali has been added 🔥🔥🔥🔥

ismartkay
Автор

Mumatha 🔥 🔥💪🔥🔥
Mukuimilira malawi guys

JANBMWSalimah
Автор

Very good very good


Thumb up 🤙 Gamba

Ngini yabho

khymanshaffieh
Автор

Big up phyzo……keep repping the ghetto and inspiring many!

Mdaphu
Автор

I dont know Y you under rated koma this is lit ❤❤❤

sheilamwalilino
Автор

inuo ndima phyzodi beat mumakupa ankolo

owenmalupiaosman
Автор

Ati chimandikumbutsa Maggie Mwauphighu😅😅

BlessieMswelo
Автор

Phyzix never disappoint 😂😂eshiii the way I love this song inee my frndz use to call me wife material 🔥🔥🙌

hildabatan
Автор

Watching this video more than 10 times.

lameckhanyezi
join shbcf.ru