MVAMA CCAP - MAPEMPHERO A M'MAWA

preview_player
Показать описание
Takulandirani ku Mapemphero a m'mawa kuno ku Mvama CCAP Church. Otsogolera mapempherowa ndi abusa Hamilton Yassin Gammah.

Mulungu akudalitseni pokhala nafe!
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

Ulariki wabwino okoma abusa. osati enawa kumangolarika zandalama

AlexKaunda-irrz
Автор

Following from capetown, you have changed my life before I thought I was a christian but wansn't after listening from your preaching now I know whom I am. Continue blessing us with words of God Rev. Yassin Gamah🙏🙏

mphatsojohnkachingwe
Автор

Amen pastor, the message is very good and touching.

JaneKaira-zm
Автор

I like your preaching, you are blessed in this field of teaching.

richardmbewe-ufzq
Автор

Powerful mumandidalitsa koposa Abusa ziphunzitso zanu nthawi zonse Ambuye apitilize mphatso ili mwayinu Amen 🙏

hestingschirwah
Автор

Wonderful preaching from you man God may almighty God help me I know who I am I by the preaching from your messenger continuing blessing him

HappyForestHills-rvgm
Автор

My life is changed because of your teaching 🙏 God blessed

RoseManzi-fteo
Автор

I like your preaching, you are a true man of God, god bless you, am from Zambia lusaka

fannyngoma
Автор

Uwu ndiye uthenga wosintha munthu. Wa ma PAPA original osati tima papa tangodzipatsati ayi. May God bless you reverend

stainbanda
Автор

Ambuye zikomo chifulukwa cha mau anuokoma am very blessed..

TamalaLungu-sq
Автор

Ambuye mulemekezeke. Uthenga umenewu ndi wanga vwandikhuza zoona

TamalaLungu-sq
Автор

Abunsa please ndi mafuna kuti ngati kungakhare kotheka ndi mafuna uthenga wambuye udzindifikira chonde Abunsa Ameen

isimailKazambe
Автор

Anthu ofunika kusafa aja koma awa, nkhawa timachira. 😂😂😂😂😅😅😅😅🤣🤣🤣🤣😁😁😁😁😛😝😋😜This man! Jesus! Jesu!

FelixMachika
Автор

Abusa timadalitsika nanu.Osati enawa mulemera miracle money

ReginaPhitso-wtjj
Автор

🎉🎉🎉❤❤❤ abusa tsegulani what's up group kuti ena aziva nawo unthenga wabwinou

PatrickHennry
Автор

Mumaudalitsa moyo wanga Mulungu apitilize kuvumbulutsa zochuluka mwa inu

gladyslingisoni
Автор

Monga upangili wachakwera it's very bad😢😢😢

PaulKaunda-ljvr