Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo

preview_player
Показать описание
On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo dreams again.

Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo walotanso.

#malawi
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

Bon umakwanila God bless you my brother

RodrickAlid
Автор

Komatu mwazi uja amaunena uja uyendadi ndithu akapanga masewera

MadalitsoChisale-jo
Автор

😂😂😂😂 umakwana wangoyenela kulota zaofesi Yako kaya wina aziti wadya chamba bola wanena kalowa kayaza 😅😅😅 the DC

chisomochavula
Автор

Koma ngumbi za ku ntcheu ndizinazina heti😅😅
Maloto sang'amba poti tikhala tchelu basi

MemoryKamanga-putj
Автор

😂😂😂😂 mpaka anakuveresani njimbo koma the DC😂😂😂😂😂

YusufuPeter
Автор

The DC woyeee mumatiyimilira inuyo musadzafe Mulungu adzangokutengani ngati mphepo yaku maloto anuwo😂😂😂

MiddayDeleza
Автор

Born Kalindo your the best keep it up brother

Chisomomataya
Автор

Go ahead kalindo ing'alule basi😂😂😂

stellacrown
Автор

Kkkkk Iwe umakwanira dziko lizikhala ndiolimba mtima osati mayesi bwana ileum wako!👍

Allanmikeyasi
Автор

Anakangokutengeratu kuti upite kumwamba koko uzikaimba hossana hossana 😂😂😂😂😂 baba prophet

AliceMbewe-yipw
Автор

Chakwela Watuwonetsa Mbonaona Zakibingo

Homeofpeace
Автор

Lero Chilimatu wamwalira, malotowa anali owona ndipo zachitika. The DC ndimachine❤❤❤❤

RiteRoderick
Автор

bon kalindo l like you all the time my brother. am watching from l85 camp

abe
Автор

koma akulu Inu mumantha zed keep it up

StuarttEphraim
Автор

Uli bhi kwambiri ndipo tikupempha ena amene amalimba mtima abwere poyera kt tizithandizana kusakhala ndimantha

EnerstMakwinja
Автор

Owe
Ndiwamisala
Chlkakhala
One
Ndinakutuluka

MartinFrakson
Автор

Moto ukunenedwawo si nyumba ya mayi kaliati yayakayo😂

stellacrown