One of my top three artist since I started follow Malawi nyuzik Tidzamuvotera is here challenging pang'ono ndi pang'ono tiyeni tiyeni ti kadikule nyimbo ndi yomweyi basi
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
InnocentKamponda
Am a strong fan for mlaka maliro, but Iam deeply disappointed with his latest decision to support a government that has led many Malawians in abject poverty. Anyway, money can do anything.
moseschihana
Tiyen team chakwela tipatse moto aliyese Ali ndi zokonda.
Alexchikweza
Nice song ndipo chovotera chilipo ndidzamuvotera
ChrifordMgwede-jggk
Am enjoying this music and the message too... Bwana mumatha kuyimba😍
yakamemes
Tikuti boma ndi lomweli sitikusintha🎉🎉
EmeliaKanyenda-zpfs
Zosinthasintha maboma tikungosaukadi.... 🎉🎉🎉🎉🎉
GraceKamanga-lh
Kutha kwa dolo, watopa mkudyesedwa ndi mkazi wake akusaka ndalama
albertharrison
Boma ndi lomweri ndithu....Chakwera is best president
innocentaponda
Mlaka mapazi ako waganiza bwanji kupanga support munthu oipa kwambili emwenso akunzunza a Malawi Koma umphawi sizinthu dikila uone chimwendo Banda akudyere nkazi wako uja funsa Dan Lu anangomudyera nkazi pano amutaya
sergiosimbi
Mulekeni Mlaka ayimbe monga mene angafinireali ndi ufulu ee ee Inu nde abwino mukupanga judge anzanu zaduuuu
shinekaipa
Mlaka maliro akungofuna chabe ndalama, munthu oti alibe qualification iliyonse wakula akudyetsedwa ndi nkazi wake or nkazi wake apakulitse banja silitha.
Charles Nsaku amangokwatilakwatila alibe kukhazikika. Oimba adyela apamalawi
End-w-uh
Mlaka ndi mlaka bas umakwana tiye nao adyere .zaphweka
MadalisoEphraim
Boma ndilomweli moto kuti more 🔥 mlaka maliro
AmaanUzair
Kusowa kosekunja kulemba nyimbo zopusa mukufuna mudyanawo misokho yathu umphawi sizithu Kupempha uku chilinga mube misokho yathu kudzela mwa mr chikangawa koma chitsilu awa anatha basi