Amene akufuna kulemba mau ot let's gather here u let's gather here 😊
MosesThomas-tgvg
Iyiyi ndi mbama yakumaliseche Bandera 🔥🔥🔥🔥
JabulanBeza-gs
Amabwera ndikhakara ndi dollar pano ndinatuluka ndipo pano siazanga ✊
BatutaMajangata-ou
This song have reminded me of a friend, Ndaziona Lingiton from Mchezi, Lilongwe. Ndimakusowa nzanga
yusuffatch
Enyaaa ngati ñzulu //
Sungabwize team yanyasuluuuu//
Nyimbo yaphwedwa🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
RealMan-kp
Jili chenene kwabasi! koma ife zimatisangalatsa heavy Akamaimba chiyao
shaik
😊😮To be flank DNA mmmmh is talented. Unique and amakhala ndima concept akeake achilendo moti eeee this is lit💥🔥why can't you be like elube my side chick
KelvinChigwadala-hd
That's an amazing improvement❤
Nice tune & great vidz❤