TONDE WADULA EPISODE 69 Full

preview_player
Показать описание
TONDE WADULA EPISODE 69 Full
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

Chufuniro amayenera kupitirira, she is a good actor. She left us too early. Will miss her tongue

justinenambazo
Автор

Pa chifuniro nde mwaiphonya magaye ma actress a sharp timangowatumiza kwina kwake not kuzima . Mbola!

godsgenerals
Автор

Aaaaa pa chifuniropo sipanayende bwino mukanamusiya kaye anali actor wa bhoooo amatisanglatsa heavy 😢😢😢

JanetJamesMachila
Автор

You guys number 1 pitilizani tonde wadula nice play watching from 🇬🇧

steriaphiri
Автор

Ndilipano kufuna kuphuzira pa muthinda ndi Gaga, mudziko lathulo alipo ambiri ochita zithu ngati anthu awiliwa keep up tonde ndikuva kukoma pano pa cape town ndikamaonera umphungu wanuwu

georgekchimwaza
Автор

Watching you makosana from South Africa Johannesburg Alberton. Sindigona kopanda kuonera seweroli guys 👏

danielantoniomsutu
Автор

kusowatu poyambira kupanga comment😅
Gaga sazatheka uyu

Komanso chifuniro samayenera kufa 😢

BonfaceMulera-pxjc
Автор

Osamayikamo za ma tsoka we are injoyong this comedy zaifa osanamizilama

BlessingsBanda-ihth
Автор

Kkkk gaga wasala pang'ono kuyaluka akungo akugozikola nkamwa kuyakhula choti uziwe chief William akuziwa kuti gaga ndi olakwa kma sakufuna kungo chulu akufuna azangwidwe azayaluke yekha

WillySitambuli
Автор

Koma gaga😂😂😂😂😂eishhh ndikusowa poyambira kulemba comment😂😂😂

EdythGloryNamponya
Автор

Chifunilo ndimusowa eshh tsinaka unja amatha ndipo ndy amabebesa 😭😭 bola adakachira ndi mole eshh amavana

BlessingsHendry
Автор

Muli bhoo guys watching from republic of 🇮🇪

jumawasi
Автор

But why chifunilo left the story early? Aaaaa will miss her seriously.

mwaiwawokazembe
Автор

Zakhwima, makwale ndi Gaga mmmm. Amfumu opusa ngati awa sindinawaone

CidrickCosmas-db
Автор

Gaga suzatheka basi😂😂😂Chifuniro wafulumira kufa 😢anali sangalatsi wanga

anniewhite
Автор

Koma mmudzi umo yha mlandu ndyosayamba😅😅😅

georgeabigailmaseko-tsfq
Автор

Mr chiphwanya mukwatire sayezi yanu, mtsikanayo mundisiyire ine😂😂😂😂boma rilowerelapo😂😂😂😂

MphatsoYusuf
Автор

Makwale wayambano kubowa ukakhala wina usinthe part yako simabeba iyaaa

JulianaChinangwa
Автор

Kd ma actor and actress akumangofah mwachisisi bwanji ku xool days mphatso disappear apaso chifuniro machaka mukuyendetsa bwanji zithuzi I think chifuniro abweratso mu njira inaaa cz January to Dec ndipatali mutiuuza zotiii chani tisanangende 👊👊

KajawoAdamBlessings
Автор

Mwalakwitsa kumuchosa chifuniro bola akachoka gaga anachenjera udyo😅

CatherineNkhoma-qp