Kalata ya Bwande Monday 23 September 2024

preview_player
Показать описание

Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

Zukuwonesa iwe ulimbali ya chikangawa 😢😢

VitumbikoKaunga
Автор

Munthu amalakwitsa or change golo anakuwa Chala mmwamba pamaso pa chakwera

SEEJSHJEFFREY
Автор

Komaa Malinga ndi udindo umene mayiyo analinawo anapeleka chiopsezo kuchipani

ChristopherChapeta
Автор

Inu nthawi zonse mumaipitsa mbiri ya DPP, sungayankhuleko mmene zinthu zikuvutira kumalawiko, kamba za likoma, kamba za kugwa kwa ndalama

frankwilliam
Автор

Komanso2 osayiwala kuti Nyama zikulu zikulu nazo zinalakwitsa malo moti apereke list ya ma udindo omwe anapereka mmalo moforokoza bwino bwino ati unduna omanga anthu

fredgabrielnyangulu
Автор

Koma vuto lakuti amene ali olimba ntima ku Malawi ndiochepa, am

NickUpoche
Автор

Inu a bwande simunayambe mwakamba chabwino cha DPP

Harrychokanda