San B - Yenda (Official Music Video)

preview_player
Показать описание
Official music video for Yenda by San B.

Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

i must mention that i am a Zambian and have loved San B's music right when he sang circular music up to the time he started singing gospel. may God continue blessing you in your music career. from pelemende to gospel honjo upto this one yenda yenda chisogolo. thank you so much San B.

philsiziya
Автор

very very Nice San b ukutiimilira heavy ndasangalala mpaka misozi

felixjohn
Автор

Amalawi akufunika kupititsa chitsogolo zitolilo zo shaaah ndayibwereza bwereza nso kuyimvera kuno kwao kwa azungu.

ramseycrown
Автор

Akulu apo mwafikapo tapitilizani makamaka mmene mwayamba kugwiritsa zitolilozo eeeh mwandifikapo ndipo mumatha boss.

ramseycrown
Автор

A byutiful song in a byutiful simple repeat.

lloydmonteiro
Автор

Komatu a San b Pena mukumationjeza kkkk Inu zanu sitinganene zambiri keep on giving us good music

vincentsegula
Автор

Mafumu is back, , , , wow apa zilibwino big up malume

brendahchikugeoffrey
Автор

San B you have done a good song to an international standard. Keep it up. Ndamva kukoma zedi.

ganizanipaul
Автор

Thanks for the massage, so helpful, may Almighty God remember you always

elisamilliward
Автор

guys this Guys knows his calling. Appreciated SAN B. i love this to the core

destergroup
Автор

San b. is some one who knows what to do

timothysakala
Автор

Wakuru awo on his own touch as usual
Great sound of malawi

frankmangoni
Автор

Musically ya work! Keep work going forward. Love your intensity!!! Seen?

Malani
Автор

Abale Ako uwadziwe... Udziweso adaniwo...

josephkanyinji
Автор

Abwana pitilizani kuponyamo tolillo, muliso ndimau abwino, omwe ndimawasilila nthawi zose, mukayamba kuimba mumasuntha moyo wanga, nyimbo zanu nayamba kuzikonda ndili wachichepere.

sbudasbabangu
Автор

Nyimbo za mkuruyu zimaveka bwino kwambiri ndizorimbikisa kwambiri

haziwellcosimas
Автор

Aliponso wina ngati?? Munthu uyu anadalisidwa👆👏👏

thomasmhango
Автор

Nyimbo yabwino koma Director zinamuvuta kwambiri munayenera kukhalamo kagulu kovina molingana ndi nyimboyi/komphunzitsidwa bwino komanso anthu/munthu ongoyimira mau oti 'yenda chitsogolo' kuonetsa zovuta zomwe akukumana nazo komabe akuyenda chitsogolo osati kumangoonetsa San B yenkha ayi chifukwa nyimbo zopanda action sizikoma bwini bwino

zombaentertainment
Автор

Lovely sound. I like all your recent videos.

graftonmanda
visit shbcf.ru