A Michael Usi Inu Si A UTM - Lyton Mangochi

preview_player
Показать описание
On Nyasa VoiceBox, Lyton Mangochi says that the Right Honourable Dr. Michael Usi is not a true member of the United Transformation Movement.

Pa Nyasa VoiceBox, Lyton Mangochi wati Wolemekezeka Dr. Michael Usi si membala weniweni wa United Transformation Movement.

#malawi
Рекомендации по теме
Комментарии
Автор

Iwe mangochi umandibowa pazambiri koma leroli wakamba chilungamo ❤❤ the spirit

BrightZionga
Автор

Munthuyu nthawi zina amalankhula zoduka mutu koma lelo walankhula chilungamo ndakukonda Mr mango hi for this audio.

MEGANABIGAILMNTHALI
Автор

This is straight forward talk and advice

shadreckphiri
Автор

Nkhani iyi ya Straight forward 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌 ulemu wanu uku kulakhura mwabnzeru manganya or tsiku limodzi lopedzeka pa mwambo oyasa ma candle yoooo or tsiku loyakhulapo zokhudza imfa ya chilimba Ambuye akukhululukireni iwe ndi mpeni othwa konse konse iiiih Chilima Rest well tidzakulirani mpaka kale 😭😭😭😭😭😭

doreenkaliati
Автор

Apapa ndiri mbariyako or mntaniwa atanva audio yakoyi akunva kukoma mot utamatero anthu akukonda kwambiri the fact u hv say to day congrats Mr Layton big up tufuna chirungamo choncho

ChristopherJohn-zz
Автор

Mwayankhula chilungamo malumee, May God bless you!!! Ameneyu adzazunzika nao mzimu wa Chilima

RitaKainga
Автор

Iwe Lyton Mangochi apa wanena mfundo osati yamasewera. Ndamvera each and every sentence looking for a mistake koma mwalankhula zaufumu weniweni.
I love you

AiwaMedia-shvx
Автор

I think you are coming back to your senses Mr Mangochi.... Keep it up.

SolomonMbewe
Автор

Galu ndi gula manganya siwa utm komaso anamupeleka chilima

mayesojameskatete
Автор

100%. Usi si wa UTM. Angofuna kusokoneza UTM yo.
Tilitonse mau olawura asiye.
Ngati zolankhura alibe angosiya. zamadirama ife sitikufuna.
Ine ndili wakwanu. Kumwitu koku Karonga. Komam'sasiye kudziwitsa anthu choonadi, monga m'nachitira pakatipa.
Tinali kuganiza kuti nanutso mwagudwa.

PollyLysonLutepo
Автор

Well composed speech keep it up Mr Mangochi. Teach him a lesson

masterchitabwino
Автор

Uthenga opanda chigamba, apa ndiye chilungamo.

peternashyo
Автор

Mr Lyton Mangochi ulemu wanu mwayankhula chilungamo God bless you Mr Mangochi

StevenGJohn
Автор

Bwana Lyton mangochi lero mwakambako mfundo zomveka bwino ulemu wanu

MadalisoKaujole
Автор

Today it's ur best audio mr mangoch best audio ever muuzenidi achose kachiwanda ka ma drama kkkk

SamangaMushe
Автор

Anali ngati Petro yemwe amamuonera Yesu patali ali pakati pa adani kumfunsa uyunso anali waiwo amvereke akunama sindikumudziwa ine ameneyo.

masterchitabwino
Автор

Ndipo bwana Mangochi mwang'alula ulemu wanu akulu awa eeeish atipepelesa sure

alexsumani
Автор

Ine umandinyasa heavy kma lero Mutu wako wayamba kugwila ntchito ❤zanzeru
Someone hit Like for me

DONNEXKhama-bkgy
Автор

Bwanji osakayendera ma office a NRB ku southern, eastern and northern regions kuti anthu alandire za unzika mu nthawi yabwino?

zulubeats
Автор

Mqngochi your right ukunena zenizeni congratulations bro

ZebronTembo-up
join shbcf.ru