A DPP Mutipanga Bwanji Convince Kuti Kuba Mumkachitila Muja Mwasiya - John Dzuwa

preview_player
Показать описание
On Nyasa VoiceBox, John Dzuwa questions how the Democratic Progressive Party (DPP) plans to convince Malawians that they have reformed and moved past their kleptocratic tendencies.

Pa Nyasa VoiceBox, John Dzuwa akufunsa momwe chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) chikufunira kukhutitsa Amalawi kuti iwo asintha ndipo asiya m'mikhalidwe yawo ya kuba.

#malawi
Комментарии
Автор

Funso la bwino kwambiri ayankhe ndithu

thulambale
Автор

Iwe wayankhula zamphamvu komanso zogwira mtima kwambiri.Anthuwa sakumangidwa pazifukwa za ndale, alidi ndi milandu yoti ayankhe, takhala tikunena kuti dpp ndi chipani chakuba kwambiri, ndalama zonsezi anayika mmatumba mwawo pano boma likusowa forex chifukwa cha kuba, ama court milandu ngati imeneyi yiziyenda mwachangu amenewa asekeledwe osawasiya iyayi.Ena azitengerapo phunziro❤❤❤

JoelKacheche-xi
Автор

😂😂😂😂😂Tikapuma kumwamba UTM my vote ❤❤❤❤❤

LinlyMathewe
Автор

Nanuso ukunama kodi thawi yonseyi anali kuti samamanga anthuwa tiyeni uko chikangawa wawononga dzikoli..

eliffagondewe
Автор

Amangidwe kumene watsa chisale mbava yayikulu imaba siwopa boma siopa polisi imachita kunene yokha kuti siwopa aliyese imangoba m, mene ingafunile amumange asiye kulankhula mopusa

MolesBrown
Автор

Manganya anathetsa banja la Ruth simika amayi adikono, vice president wamoyo wakupha

Homeofpeace