Sangie ndi vibe kwambiri🙌🙌🙌. Sungaonere part yoti pali sangie munthu osasekai. Ahhhh bigup Sangie. Ahhh ndakutaira mitengo yonse🙌🙌🙌🙌
zirwachannelyewofficial
Ndipo chomwe chandisangalatsa pa Usauver ndichoti yayambira pomwe inathera 5 ndipo muzitero guys keep high high
fredgabrielnyangulu
Amene timayembekezera kut hyphen amupezelera mkazi wake ndi Mashasi tikweze manja😂😂😂😂😂😂😂😂
AbelMchema
Let's gather here for ganizani 🔥🔥🔥🔥this dude is so protective 🙌
MikaRyt
Emmie ya sugar Mamie akuyitha, sangie is just the best, Gani is very natural excellent. Keep it up guys and kamwana kaja kakuitha heavy
benmasache
Patricia and Ganizan acting ili good heavy, big up guys🙏
IsaacKanyamula-idju
Ganizani akhale ambassador # take care for young girls
edwardcruz
Kma sangie🤣🤣🙌 nde it's the song for me and I like ganizani too, he is a natural
cynthiachirwa
This episode deserves an award for sure. Big up guys. You are improving in each episode. I'm casting my flowers to the whole crew starting from the camera handlers 🎉🔥💯
nomiekawawa
Ine Gani amandiwaza😂😂😂. He is so calm koma zimayankhulidwazo🙌🙌
BlklilSis
Best comedy ever 🎉 koma muja anapangira MPUGWEPU kuopseza a shadow asadzabwerezeso fukwa ineso ndnachita nawo mantha 😂😂😂😂
PhilimoniEphraim
Iyi nde best ever eeh yachuluka fans bwino....
arthurAlfazemakondesi
Ganizani ndi actor mbambane uyu anakonza
harrisonmanyika
Keep it up guys camera kuposa tv ya bomatu koma ganizani machine ❤
christophermkhize
Nkhani ya kobwe yokhayo ngakhale ine nditha kulowa fast yosafunatu until khobwe athere2 mnyumba 😂😂. #pat#Gan# Ngozo achita kuthawira2 serie yonse osaonekako kuzemba ndiwo khobwe.❤much love from South Africa guys mumatha.
HopsyA-mxnm
Km Patricia wandsekesa pakat pa usiku ndipo ndmangobwerez pamodz pompo ' akaxi awo amenewo, akazi awo atsopano, akuziwan nd matious, 🤣🤣🤣🤣 nsaname keep the fire burning, moto kuti 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
MercyTemboh
I just love this episode 😍, hyphen adzafa ndi BP tu akangodziwa🤣🤣🤣
MaureenMussah
Patricia n Ganizani eeee u but the song hits so hard in my heart😢😢
DebraChimbaka
And the song at the end is so nice, simungatuluse
GeoffSande
I saw Ganizani at Kamuzu stadium. Dazi lija ndizazenizeni eti, ndimaona ngati ndimu usauver mokhamu