Secretary General Wa chipani cholamula wakumana nazotu ku Blantyre 🙌💔

preview_player
Показать описание
#politics #malawi #africa #trending #fypシ゚viral #memes
Комментарии
Автор

Achimwendo chilichose Dpp osayankhula zamavuto omwe anthu akukumananawo bwanji

YusufMoyo
Автор

Vuto la anthu awa akulimbana ndi APM instead of kut aziyakhula fundo zothandiza a Malawi mmmxxwie mbudzi za anthu

LeyvanSamuel-petc
Автор

Chimwendo akuona ngati wozindikila alipo yekha aziona

paulmanyamba
Автор

Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

BENSONRANGWANI
Автор

Aziyakhula mavuto omwe alipo osati kumangoyakhula za DPP. Chomwe tufuna ife fertilizer tidzigula motchipa at least 40-50 pin

TachikoMwanamanga
Автор

"Mzimu wa a Gadama, mzimu wa a Chiwanga...amafuna kuti tidziwe.."Lucius Banda.

jesusminded
Автор

Munthu wokula mutuyo chisilu ndichomwe chimamuipisira mbiri chakwera ine ndimanena nthawi zambiri kuti chakwera anali muthu wabwino vuto anatenga mphavu ku MCP

NgongireMwakasungula
Автор

Wagwanayo galu iwe 😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅umana ngati timadya pakhomo pako kuti tizikuyankha wanyowatu chimutu ukula ngati mpombe mwamuchita bwino guys

SanudiMcDonald
Автор

ndugwilizana ndizomwe aku nena bambo wavala Vest ya Blue ndichipewawo osati Chimutu Banda🙄

LloydChiposa
Автор

Ati pamene makanja ndi Black missionaries akukonzeka kuti atiyankhule😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

Kabwilachikangawa
Автор

APM my vote inu bachedwani mkuenda ndi makanja wanuyo

Biath-mb
Автор

Muziyankhula zothandiza a MW osati za DPP

ShillahLawrence
Автор

Chimwendo tatiuzeni za fertilizer kuti zili pata namachende iwe

DanielDoctor-tp
Автор

Akulimbana ndiza Dpp koma Iwo Ali pa mpando bwanji osasova mabvuto aMalawi..kuli njala anthu akudya chiteze.. fertilizer, chimanga..sizikuoneka koma kuchikamwa kukhalira kukamba za Dpp..ndipo iwe Chilundi ukuzimva kwa basi ndi misonkho yathu Chimutuu 😮😮😮

CharityMhone-ukym
Автор

😂😂😂 anthu sadya ma Director bibi la anthu

frasersuman
Автор

Kodi olo deputy presidentiyo Ku Malawi kuno adzigwila ntchito yanji?pakuti tili ndizitsanzo za Kassim Chilumpha, Joyce Banda, a Chilima ndi a Peter, komanso a Chakwera ndi a Chilima komanso a Joyce ndi a Bingu, Zomwe zikuonesa kuti VP Ku MW alibe ntchito

ShillahLawrence
Автор

Iwe kuyowoyachika khalawaka pasi chimwendo

kondwamlungu
Автор

😂😂😂😂😂Amalawi sianthu wamba, anatopa ndipo sizikuwakhuza

SteynMaduka
Автор

Anthu sizikuwakhudza.
😂😂😂😂 Za Manyazi 😂

MandalaChaona
Автор

😂😂😂😂😂😂😂😂mapwalaako zimenezo ndifundo zowauza anthu nsokhano ulionse nfundo zako zolimbana ndi dpp basi

EmmanuelRichard-kk